Yesaya 5:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndamva Yehova wa makamu akulumbira kuti nyumba zambiri, ngakhale zitakhala zikuluzikulu ndiponso zabwino, zidzakhala chinthu chodabwitsa kwambiri ndipo zidzakhala zopanda wokhalamo.+
9 Ndamva Yehova wa makamu akulumbira kuti nyumba zambiri, ngakhale zitakhala zikuluzikulu ndiponso zabwino, zidzakhala chinthu chodabwitsa kwambiri ndipo zidzakhala zopanda wokhalamo.+