Salimo 50:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mulungu wathu adzabwera ndipo sadzakhala chete.+Pamaso pake pali moto wonyeketsa,+Ndipo pamalo onse omuzungulira pali mkuntho wamphamvu.+ Yesaya 43:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Komanso, nthawi zonse ine sindisintha.+ Palibenso wina amene angathe kupulumutsa anthu m’dzanja langa.+ Ndikayamba kuchitapo kanthu,+ ndani amene angalimbane ndi dzanja langa?”+ Yeremiya 5:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Kodi sindiyenera kuwalanga chifukwa cha zinthu zimenezi?” watero Yehova.+ “Kapena kodi sindiyenera kubwezera mtundu wa anthu amakhalidwe oterewa?”+
3 Mulungu wathu adzabwera ndipo sadzakhala chete.+Pamaso pake pali moto wonyeketsa,+Ndipo pamalo onse omuzungulira pali mkuntho wamphamvu.+
13 “Komanso, nthawi zonse ine sindisintha.+ Palibenso wina amene angathe kupulumutsa anthu m’dzanja langa.+ Ndikayamba kuchitapo kanthu,+ ndani amene angalimbane ndi dzanja langa?”+
9 “Kodi sindiyenera kuwalanga chifukwa cha zinthu zimenezi?” watero Yehova.+ “Kapena kodi sindiyenera kubwezera mtundu wa anthu amakhalidwe oterewa?”+