Yobu 9:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndithu iye amalanda. Ndani angamuletse?Ndani angamufunse kuti, ‘Mukuchita chiyani?’+ Yesaya 14:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pakuti Yehova wa makamu wagamula,+ ndani angazilepheretse?+ Dzanja lake n’limene latambasuka, ndani angalibweze?+
27 Pakuti Yehova wa makamu wagamula,+ ndani angazilepheretse?+ Dzanja lake n’limene latambasuka, ndani angalibweze?+