Salimo 50:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Wachita zinthu zonsezi, koma ine ndinakhala chete.+Unali kuganiza kuti ine ndikhala ngati iwe.+Ine ndidzakudzudzula,+ ndipo ndidzaika machimo ako onse poyera iwe ukuona.+ Yeremiya 16:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Chotero ndisanawabwezeretse, ndidzawabwezera zolakwa zawo zonse+ ndi machimo awo onse chifukwa choipitsa dziko langa.+ Anadzaza cholowa changa ndi mitembo ya zinthu zawo zochititsa mseru ndiponso zinthu zawo zonyansazo.’”+ Ezekieli 11:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “‘“Koma amene akuumirira mafano awo onyansa ndi zinthu zawo zonyansa,+ ndidzawabwezera monga mwa njira zawo,” watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.’”+ Yoweli 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Tsopano ndili nawenso chiyani iwe Turo ndi Sidoni+ ndiponso inu nonse okhala m’chigawo cha Filisitiya?+ Kodi zimenezi ndi zimene mukundipatsa monga mphoto yanga? Ngati mukundipatsa zimenezi, ine ndidzakubwezerani mwamsanga ndiponso mofulumira zimene mwandichitirazo.+
21 Wachita zinthu zonsezi, koma ine ndinakhala chete.+Unali kuganiza kuti ine ndikhala ngati iwe.+Ine ndidzakudzudzula,+ ndipo ndidzaika machimo ako onse poyera iwe ukuona.+
18 Chotero ndisanawabwezeretse, ndidzawabwezera zolakwa zawo zonse+ ndi machimo awo onse chifukwa choipitsa dziko langa.+ Anadzaza cholowa changa ndi mitembo ya zinthu zawo zochititsa mseru ndiponso zinthu zawo zonyansazo.’”+
21 “‘“Koma amene akuumirira mafano awo onyansa ndi zinthu zawo zonyansa,+ ndidzawabwezera monga mwa njira zawo,” watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.’”+
4 “Tsopano ndili nawenso chiyani iwe Turo ndi Sidoni+ ndiponso inu nonse okhala m’chigawo cha Filisitiya?+ Kodi zimenezi ndi zimene mukundipatsa monga mphoto yanga? Ngati mukundipatsa zimenezi, ine ndidzakubwezerani mwamsanga ndiponso mofulumira zimene mwandichitirazo.+