Amosi 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndidzatumiza moto pakhoma la Turo ndipo udzanyeketsa nsanja zake zokhalamo.’+ Aroma 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye adzaweruza aliyense malinga ndi ntchito zake motere:+