Salimo 50:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Akuitana kumwamba ndi dziko lapansi+Kuti apereke chiweruzo kwa anthu ake. Iye akuti:+ Mlaliki 12:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pakuti Mulungu woona adzaweruza ntchito iliyonse ndiponso chinthu chilichonse chobisika, kuti aone ngati zili zabwino kapena zoipa.+
14 Pakuti Mulungu woona adzaweruza ntchito iliyonse ndiponso chinthu chilichonse chobisika, kuti aone ngati zili zabwino kapena zoipa.+