Yesaya 23:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Iye wati: “Usadzakondwerenso+ namwaliwe, mwana wamkazi wa Sidoni+ woponderezedwa. Nyamuka, wolokera ku Kitimu.+ Koma ngakhale kumeneko, sukapezako mpumulo.” Zekariya 9:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mawu amenewa akuweruzanso Hamati+ amene anachita naye malire. Komanso akuweruza Turo+ ndi Sidoni+ chifukwa ali ndi nzeru zambiri.+
12 Iye wati: “Usadzakondwerenso+ namwaliwe, mwana wamkazi wa Sidoni+ woponderezedwa. Nyamuka, wolokera ku Kitimu.+ Koma ngakhale kumeneko, sukapezako mpumulo.”
2 Mawu amenewa akuweruzanso Hamati+ amene anachita naye malire. Komanso akuweruza Turo+ ndi Sidoni+ chifukwa ali ndi nzeru zambiri.+