Ezekieli 26:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “‘Ndidzathetsa phokoso la kuimba kwako+ ndipo phokoso la azeze ako silidzamvekanso.+