Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 23:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 “Iwe hule amene unaiwalidwa, tenga zeze n’kumazungulira mumzinda.+ Yesetsa kuimba zezeyo mwaluso. Imba nyimbo zambiri kuti ukumbukiridwe.”

  • Yesaya 24:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Nyimbo zachisangalalo zoimbidwa ndi maseche zasiya kumveka. Phokoso la anthu okondwa kwambiri silikumvekanso. Nyimbo zachisangalalo zoimbidwa ndi zeze zaleka kumveka.+

  • Chivumbulutso 18:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Pamenepo kuimba kwa oimba motsagana ndi zeze, kwa oimba zitoliro, kwa oimba malipenga, ndi kwa oimba ena, sikudzamvekanso+ mwa iwe. Mwa iwe simudzapezekanso mmisiri wa ntchito iliyonse, ngakhale phokoso la mphero silidzamvekanso mwa iwe.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena