-
Yesaya 23:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 “Iwe hule amene unaiwalidwa, tenga zeze nʼkumazungulira mumzinda.
Imba zeze wakoyo mwaluso.
Imba nyimbo zambiri,
Kuti anthu akukumbukire.”
-