Yesaya 23:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Iwe hule amene unaiwalidwa, tenga zeze n’kumazungulira mumzinda.+ Yesetsa kuimba zezeyo mwaluso. Imba nyimbo zambiri kuti ukumbukiridwe.” Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:16 Yesaya 1, ptsa. 253-254
16 “Iwe hule amene unaiwalidwa, tenga zeze n’kumazungulira mumzinda.+ Yesetsa kuimba zezeyo mwaluso. Imba nyimbo zambiri kuti ukumbukiridwe.”