Miyambo 7:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndinaona mkazi akubwera kudzakumana naye atavala zovala zosonyeza kuti ndi hule.+ Mkaziyo anali wamtima wachinyengo, Yeremiya 30:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Achigololo onse amene anali kukukonda kwambiri akuiwala.+ Iwo sakukufunafunanso. Ndakumenya ndi mkwapulo+ ngati mdani ndipo ndakulanga ngati munthu wankhanza+ chifukwa cha kuchuluka kwa zolakwa zako.+ Machimo ako achuluka kwambiri.+
10 Ndinaona mkazi akubwera kudzakumana naye atavala zovala zosonyeza kuti ndi hule.+ Mkaziyo anali wamtima wachinyengo,
14 Achigololo onse amene anali kukukonda kwambiri akuiwala.+ Iwo sakukufunafunanso. Ndakumenya ndi mkwapulo+ ngati mdani ndipo ndakulanga ngati munthu wankhanza+ chifukwa cha kuchuluka kwa zolakwa zako.+ Machimo ako achuluka kwambiri.+