Yesaya 14:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kunyada kwako kwatsikira ku Manda limodzi ndi phokoso la zoimbira zako za zingwe.+ Mphutsi zayalana pansi pako ngati bedi, ndipo nyongolotsi zasanduka chofunda chako.’+
11 Kunyada kwako kwatsikira ku Manda limodzi ndi phokoso la zoimbira zako za zingwe.+ Mphutsi zayalana pansi pako ngati bedi, ndipo nyongolotsi zasanduka chofunda chako.’+