Yobu 17:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndidzaitana dzenje+ kuti, ‘Ndinu bambo anga!’Kwa mphutsi+ ndidzati, ‘Mayi anga ndi mlongo wanga!’ Yobu 24:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mimba idzamuiwala, mphutsi zidzamumva kutsekemera pomuyamwa,+Ndipo iye sadzakumbukiridwanso.+Kupanda chilungamo kudzathyoledwa ngati mtengo.+
20 Mimba idzamuiwala, mphutsi zidzamumva kutsekemera pomuyamwa,+Ndipo iye sadzakumbukiridwanso.+Kupanda chilungamo kudzathyoledwa ngati mtengo.+