Miyambo 10:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anthu akamakumbukira zabwino zimene munthu wolungama anali kuchita, amam’dalitsa,+ koma dzina la anthu oipa lidzawola.+ Mlaliki 8:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma ngakhale zili choncho, ndaona anthu oipa akuikidwa m’manda.+ Ndaonanso mmene iwo anabwerera ndi mmene anachokera pamalo oyera,+ n’kuiwalika mumzinda umene anali kuchitiramo zoipazo.+ Izinso n’zachabechabe. Mlaliki 9:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pakuti amoyo amadziwa kuti adzafa,+ koma akufa sadziwa chilichonse.+ Iwo salandiranso malipiro alionse, chifukwa zonse zimene anthu akanawakumbukira nazo zaiwalika.+
7 Anthu akamakumbukira zabwino zimene munthu wolungama anali kuchita, amam’dalitsa,+ koma dzina la anthu oipa lidzawola.+
10 Koma ngakhale zili choncho, ndaona anthu oipa akuikidwa m’manda.+ Ndaonanso mmene iwo anabwerera ndi mmene anachokera pamalo oyera,+ n’kuiwalika mumzinda umene anali kuchitiramo zoipazo.+ Izinso n’zachabechabe.
5 Pakuti amoyo amadziwa kuti adzafa,+ koma akufa sadziwa chilichonse.+ Iwo salandiranso malipiro alionse, chifukwa zonse zimene anthu akanawakumbukira nazo zaiwalika.+