Yobu 24:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mimba idzamuiwala, mphutsi zidzamumva kutsekemera pomuyamwa,+Ndipo iye sadzakumbukiridwanso.+Kupanda chilungamo kudzathyoledwa ngati mtengo.+ Yesaya 14:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kunyada kwako kwatsikira ku Manda limodzi ndi phokoso la zoimbira zako za zingwe.+ Mphutsi zayalana pansi pako ngati bedi, ndipo nyongolotsi zasanduka chofunda chako.’+ Maliko 9:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 kumene mphutsi za mitembo sizifa ndipo moto wake suzima.+
20 Mimba idzamuiwala, mphutsi zidzamumva kutsekemera pomuyamwa,+Ndipo iye sadzakumbukiridwanso.+Kupanda chilungamo kudzathyoledwa ngati mtengo.+
11 Kunyada kwako kwatsikira ku Manda limodzi ndi phokoso la zoimbira zako za zingwe.+ Mphutsi zayalana pansi pako ngati bedi, ndipo nyongolotsi zasanduka chofunda chako.’+