Chivumbulutso 18:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pamenepo kuimba kwa oimba motsagana ndi zeze, kwa oimba zitoliro, kwa oimba malipenga, ndi kwa oimba ena, sikudzamvekanso+ mwa iwe. Mwa iwe simudzapezekanso mmisiri wa ntchito iliyonse, ngakhale phokoso la mphero silidzamvekanso mwa iwe.
22 Pamenepo kuimba kwa oimba motsagana ndi zeze, kwa oimba zitoliro, kwa oimba malipenga, ndi kwa oimba ena, sikudzamvekanso+ mwa iwe. Mwa iwe simudzapezekanso mmisiri wa ntchito iliyonse, ngakhale phokoso la mphero silidzamvekanso mwa iwe.