Salimo 30:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Inu Yehova, mwanditulutsa m’Manda,+Mwandisunga ndi moyo, kuti ndisatsikire m’dzenje.+ Salimo 49:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kuti akhale ndi moyo mpaka muyaya osaona dzenje la manda.+ Salimo 143:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Fulumirani, ndiyankheni inu Yehova.+Mphamvu zanga zatha.+Musandibisire nkhope yanu,+Chifukwa mukatero ndikhala ngati anthu amene akutsikira kudzenje la manda.+ Miyambo 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tiye tikawameze amoyo+ ngati mmene amachitira Manda,*+ tikawameze athunthu ngati amene akupita kudzenje.+ Yesaya 14:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Koma adzakutsitsira ku Manda,+ pansi penipeni pa dzenje.+ Yona 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndinatsikira m’tsinde mwenimweni mwa mapiri.Zotsekera za dziko lapansi zinanditsekereza kuti ndikhale komweko mpaka kalekale.*Koma inu Yehova Mulungu wanga, munanditulutsa m’dzenje ndili wamoyo.+
7 Fulumirani, ndiyankheni inu Yehova.+Mphamvu zanga zatha.+Musandibisire nkhope yanu,+Chifukwa mukatero ndikhala ngati anthu amene akutsikira kudzenje la manda.+
12 Tiye tikawameze amoyo+ ngati mmene amachitira Manda,*+ tikawameze athunthu ngati amene akupita kudzenje.+
6 Ndinatsikira m’tsinde mwenimweni mwa mapiri.Zotsekera za dziko lapansi zinanditsekereza kuti ndikhale komweko mpaka kalekale.*Koma inu Yehova Mulungu wanga, munanditulutsa m’dzenje ndili wamoyo.+