Luka 10:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Iwenso Kaperenao, kodi udzakwezedwa kumwamba kapena?+ Ku Manda*+ n’kumene udzatsikira ndithu! Luka 14:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pakuti aliyense wodzikweza adzatsitsidwa, ndipo wodzichepetsa adzakwezedwa.”+