Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 9:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Anthu oipa+ adzapita ku Manda,+

      Ngakhalenso anthu onse a mitundu ina amene aiwala Mulungu.+

  • Yesaya 14:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 “Koma adzakutsitsira ku Manda,+ pansi penipeni pa dzenje.+

  • Ezekieli 26:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 ndidzakutsitsira m’dzenje, ngati mmene ndinatsitsira ena onse m’manda momwe muli anthu amene anafa kalekale.+ Ine ndidzakuchititsa kukhala pansi, panthaka.+ Udzakhala kumeneko pamodzi ndi malo ena amene anawonongedwa kalekale ndiponso pamodzi ndi ena onse amene akutsikira kumanda.+ Ndidzachita zimenezi kuti anthu asadzakhalenso mwa iwe, koma m’dziko la anthu amoyo ndidzaikamo zokongoletsera.+

  • Mateyu 11:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Iwenso Kaperenao,+ kodi udzakwezedwa kumwamba kapena? Ku Manda*+ n’kumene udzatsikira ndithu,+ chifukwa ntchito zamphamvu zimene zinachitika mwa iwe zikanachitika ku Sodomu, mzindawo ukanakhala ulipobe mpaka lero.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena