Salimo 143:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Fulumirani, ndiyankheni inu Yehova.+Mphamvu zanga zatha.+Musandibisire nkhope yanu,+Chifukwa mukatero ndikhala ngati anthu amene akutsikira kudzenje la manda.+ Ezekieli 28:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Adzakutsitsira kudzenje.+ Udzafa ngati munthu wophedwa ndi lupanga pakatikati pa nyanja.+ Luka 10:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Iwenso Kaperenao, kodi udzakwezedwa kumwamba kapena?+ Ku Manda*+ n’kumene udzatsikira ndithu!
7 Fulumirani, ndiyankheni inu Yehova.+Mphamvu zanga zatha.+Musandibisire nkhope yanu,+Chifukwa mukatero ndikhala ngati anthu amene akutsikira kudzenje la manda.+