Deuteronomo 32:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pakuti pa kukwiya kwanga moto wayaka,+Ndipo udzayaka mpaka kukafika ku Manda,* malo a pansi penipeni.+Udzanyeketsa dziko lapansi ndi zipatso zake,+Ndi kuyatsa maziko a mapiri.+ Salimo 88:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mwandiika m’dzenje lakuya kwambiri,M’malo a mdima, m’phompho lalikulu.+ Ezekieli 32:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Iwe mwana wa munthu, lirira khamu la ku Iguputo ndi kulengeza kuti lidzatsikira kumanda.+ Dzikolo ndi anthu a mitundu yamphamvu adzatsikira pansi pa nthaka+ limodzi ndi amene akutsikira kudzenje.+
22 Pakuti pa kukwiya kwanga moto wayaka,+Ndipo udzayaka mpaka kukafika ku Manda,* malo a pansi penipeni.+Udzanyeketsa dziko lapansi ndi zipatso zake,+Ndi kuyatsa maziko a mapiri.+
18 “Iwe mwana wa munthu, lirira khamu la ku Iguputo ndi kulengeza kuti lidzatsikira kumanda.+ Dzikolo ndi anthu a mitundu yamphamvu adzatsikira pansi pa nthaka+ limodzi ndi amene akutsikira kudzenje.+