-
Ezekieli 31:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Choncho sipadzakhalanso mtengo uliwonse wothiriridwa bwino umene udzakhale wautali kwambiri kapena umene nsonga zake zidzafike m’mitambo. Sipadzakhala mtengo uliwonse umene uli pamadzi ambiri umene udzatalike kukafika m’mitambo, pakuti mitengo yonse idzakhala itadulidwa.+ Yonse idzakhala itatsikira pansi pa nthaka+ pamodzi ndi ana a anthu amene akutsikira kudzenje.’
-