Salimo 21:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mudzawakhalitsa ngati oponyedwa mung’anjo yamoto pa nthawi ya kuonekera kwanu.+Yehova adzawameza mu mkwiyo wake, ndipo moto udzawanyeketsa.+ Yeremiya 15:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndidzachititsa adani anu kutenga chumacho ndi kupita nacho kudziko limene simukulidziwa,+ pakuti mkwiyo wanga wayatsa moto.+ Ndithu, moto wakuyakirani anthu inu.” Maliro 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yehova wasonyeza ukali wake wonse.+ Wakhuthula mkwiyo wake woyaka moto.+Iye wayatsa moto m’Ziyoni, umene wanyeketsa maziko ake.+
9 Mudzawakhalitsa ngati oponyedwa mung’anjo yamoto pa nthawi ya kuonekera kwanu.+Yehova adzawameza mu mkwiyo wake, ndipo moto udzawanyeketsa.+
14 Ndidzachititsa adani anu kutenga chumacho ndi kupita nacho kudziko limene simukulidziwa,+ pakuti mkwiyo wanga wayatsa moto.+ Ndithu, moto wakuyakirani anthu inu.”
11 Yehova wasonyeza ukali wake wonse.+ Wakhuthula mkwiyo wake woyaka moto.+Iye wayatsa moto m’Ziyoni, umene wanyeketsa maziko ake.+