Deuteronomo 32:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pakuti pa kukwiya kwanga moto wayaka,+Ndipo udzayaka mpaka kukafika ku Manda,* malo a pansi penipeni.+Udzanyeketsa dziko lapansi ndi zipatso zake,+Ndi kuyatsa maziko a mapiri.+ Yesaya 42:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Choncho Mulungu anali kuwakhuthulira mkwiyo, ukali wake, ndi nkhondo yoopsa.+ Nkhondoyo inali kuwapsereza+ koma iwo sanazindikire.+ Inapitiriza kuwatentha koma iwo sanaganizire chilichonse mumtima mwawo.+ Aheberi 12:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Pakuti Mulungu wathu alinso moto wowononga.+
22 Pakuti pa kukwiya kwanga moto wayaka,+Ndipo udzayaka mpaka kukafika ku Manda,* malo a pansi penipeni.+Udzanyeketsa dziko lapansi ndi zipatso zake,+Ndi kuyatsa maziko a mapiri.+
25 Choncho Mulungu anali kuwakhuthulira mkwiyo, ukali wake, ndi nkhondo yoopsa.+ Nkhondoyo inali kuwapsereza+ koma iwo sanazindikire.+ Inapitiriza kuwatentha koma iwo sanaganizire chilichonse mumtima mwawo.+