Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 26:38
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 38 Mudzatheratu pakati pa anthu a mitundu ina,+ ndipo dziko la adani anu lidzakumezani.

  • Yeremiya 16:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Choncho ndidzakutayani kunja kukuchotsani m’dziko lino+ ndi kukupititsani kudziko limene inu ngakhalenso makolo anu sanalidziwe.+ Kumeneko mukatumikira milungu ina+ usana ndi usiku chifukwa sindidzakumverani chifundo.”’

  • Yeremiya 17:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Mwa kufuna kwanu munataya cholowa chimene ndinakupatsani.+ Inenso ndidzakuchititsani kutumikira adani anu m’dziko limene simunalidziwe.+ Anthu inu, ndakuyatsani ndi mkwiyo wanga+ ndipo moto wake udzayakabe mpaka kalekale.”

  • Amosi 5:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Pakuti ndidzakupititsani ku ukapolo, kutali kwambiri ndi ku Damasiko,’+ watero Mulungu wa makamu, amene dzina lake ndi Yehova.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena