Deuteronomo 28:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Yehova adzakuyendetsa+ pamodzi ndi mfumu+ yako imene udzadziikira, kukupititsa ku mtundu umene iweyo kapena makolo ako simunaudziwe. Kumeneko udzatumikira milungu ina, yamtengo kapena yamwala.+ 2 Mbiri 7:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 ineyo ndidzakuchotsani padziko langa limene ndakupatsani+ ndipo nyumba iyi yomwe ndaiyeretsa+ chifukwa cha dzina langa, ndidzaichotsa pamaso panga.+ Ndidzachititsa anthu kuipekera mwambi+ ndi kuitonza pakati pa mitundu yonse ya anthu.+
36 Yehova adzakuyendetsa+ pamodzi ndi mfumu+ yako imene udzadziikira, kukupititsa ku mtundu umene iweyo kapena makolo ako simunaudziwe. Kumeneko udzatumikira milungu ina, yamtengo kapena yamwala.+
20 ineyo ndidzakuchotsani padziko langa limene ndakupatsani+ ndipo nyumba iyi yomwe ndaiyeretsa+ chifukwa cha dzina langa, ndidzaichotsa pamaso panga.+ Ndidzachititsa anthu kuipekera mwambi+ ndi kuitonza pakati pa mitundu yonse ya anthu.+