Deuteronomo 4:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 ndikutenga kumwamba ndi dziko lapansi+ lero monga mboni zokutsutsani, kuti mudzafafanizidwa mwamsanga m’dziko limene mukupita kukalitenga mutawoloka Yorodano. Simudzatalikitsa masiku anu m’dzikomo chifukwa mudzawonongedwa ndithu.+ 2 Mafumu 17:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Chotero Yehova anakana mbewu yonse+ ya Isiraeli ndipo anawasautsa n’kuwapereka m’manja mwa olanda katundu, mpaka iye anawathamangitsa pamaso pake.+
26 ndikutenga kumwamba ndi dziko lapansi+ lero monga mboni zokutsutsani, kuti mudzafafanizidwa mwamsanga m’dziko limene mukupita kukalitenga mutawoloka Yorodano. Simudzatalikitsa masiku anu m’dzikomo chifukwa mudzawonongedwa ndithu.+
20 Chotero Yehova anakana mbewu yonse+ ya Isiraeli ndipo anawasautsa n’kuwapereka m’manja mwa olanda katundu, mpaka iye anawathamangitsa pamaso pake.+