Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 25:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Iwo anapha ana a Zedekiya iye akuona,+ kenako Zedekiyayo anam’chititsa khungu.+ Atatero anamumanga ndi maunyolo amkuwa+ n’kupita naye ku Babulo.+

  • 2 Mbiri 33:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Pomalizira pake Yehova anawabweretsera+ akuluakulu a asilikali a mfumu ya Asuri.+ Iwo anagwira Manase akubisala m’dzenje.+ Atatero anam’manga+ ndi zomangira ziwiri zamkuwa n’kupita naye ku Babulo.

  • 2 Mbiri 36:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Kenako Nebukadinezara+ mfumu ya Babulo anabwera+ kudzam’manga ndi zomangira ziwiri zamkuwa n’kupita naye ku Babulo.+

  • Yeremiya 22:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Ponena za Salumu+ mwana wa Yosiya, mfumu ya Yuda, amene akulamulira m’malo mwa bambo ake Yosiya,+ amene anachoka m’dziko lino kupita ku ukapolo, Yehova wanena kuti, ‘Sadzabwereranso kwawo,

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena