Yobu 36:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Anthu akamangidwa m’matangadza,+Amagwidwa ndi zingwe za masautso. Salimo 107:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ena anali kukhala mu mdima, mu mdima wandiweyani,+Anali akaidi osautsika ndi omangidwa maunyolo,+