Salimo 107:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ena anali kukhala mu mdima, mu mdima wandiweyani,+Anali akaidi osautsika ndi omangidwa maunyolo,+