Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mbiri 33:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Pomalizira pake Yehova anawabweretsera+ akuluakulu a asilikali a mfumu ya Asuri.+ Iwo anagwira Manase akubisala m’dzenje.+ Atatero anam’manga+ ndi zomangira ziwiri zamkuwa n’kupita naye ku Babulo.

  • Yobu 36:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Anthu akamangidwa m’matangadza,+

      Amagwidwa ndi zingwe za masautso.

  • Salimo 105:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Kumeneko anasautsa mapazi ake ndi matangadza,+

      Anam’manga ndi maunyolo.+

  • Salimo 149:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Ndiponso kuti amange mafumu awo maunyolo,+

      Ndi kumanga anthu awo olemekezeka m’matangadza achitsulo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena