Deuteronomo 28:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Yehova adzakuthamangitsani limodzi ndi mfumu yanu imene mudzaike kuti izikulamulirani, kukupititsani ku mtundu umene inuyo kapena makolo anu sanaudziwe.+ Kumeneko mudzatumikira milungu ina, milungu yamtengo ndi yamwala.+ Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 28:36 Ulosi wa Danieli, ptsa. 71-72
36 Yehova adzakuthamangitsani limodzi ndi mfumu yanu imene mudzaike kuti izikulamulirani, kukupititsani ku mtundu umene inuyo kapena makolo anu sanaudziwe.+ Kumeneko mudzatumikira milungu ina, milungu yamtengo ndi yamwala.+