Yeremiya 15:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndidzachititsa adani anu kutenga chumacho ndi kupita nacho kudziko limene simukulidziwa,+ pakuti mkwiyo wanga wayatsa moto.+ Ndithu, moto wakuyakirani anthu inu.” Yeremiya 17:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mwa kufuna kwanu munataya cholowa chimene ndinakupatsani.+ Inenso ndidzakuchititsani kutumikira adani anu m’dziko limene simunalidziwe.+ Anthu inu, ndakuyatsani ndi mkwiyo wanga+ ndipo moto wake udzayakabe mpaka kalekale.”
14 Ndidzachititsa adani anu kutenga chumacho ndi kupita nacho kudziko limene simukulidziwa,+ pakuti mkwiyo wanga wayatsa moto.+ Ndithu, moto wakuyakirani anthu inu.”
4 Mwa kufuna kwanu munataya cholowa chimene ndinakupatsani.+ Inenso ndidzakuchititsani kutumikira adani anu m’dziko limene simunalidziwe.+ Anthu inu, ndakuyatsani ndi mkwiyo wanga+ ndipo moto wake udzayakabe mpaka kalekale.”