Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 29:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Pamenepo mkwiyo wa Yehova unayakira dziko limeneli mwa kulibweretsera matemberero onse olembedwa m’buku ili.+

  • Yesaya 5:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 N’chifukwa chake mkwiyo wa Yehova wayakira anthu ake ndipo adzatambasula dzanja lake n’kuwapha.+ Mapiri adzanjenjemera+ ndipo mitembo yawo idzakhala ngati zinyalala m’misewu.+

      Chifukwa cha zonsezi, mkwiyo wake sunabwerere, ndipo dzanja lake lidakali lotambasula.

  • Yeremiya 15:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Ndidzachititsa adani anu kutenga chumacho ndi kupita nacho kudziko limene simukulidziwa,+ pakuti mkwiyo wanga wayatsa moto.+ Ndithu, moto wakuyakirani anthu inu.”

  • Nahumu 1:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Iye atapsa mtima, ndani angaime pamaso pake?+ Iye atakwiya, ndani angalimbe mtima kuima pamaso pake?+

      Mkwiyo wake adzaukhuthula ngati moto+ ndipo miyala idzagwetsedwa chifukwa cha iye.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena