Deuteronomo 32:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pakuti pa kukwiya kwanga moto wayaka,+Ndipo udzayaka mpaka kukafika ku Manda,* malo a pansi penipeni.+Udzanyeketsa dziko lapansi ndi zipatso zake,+Ndi kuyatsa maziko a mapiri.+ Chivumbulutso 16:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kenako, ndinamva mawu ofuula+ ochokera m’malo opatulika akuuza angelo 7 aja kuti: “Pitani, kathireni mbale 7 za mkwiyo+ wa Mulunguzo kudziko lapansi.”
22 Pakuti pa kukwiya kwanga moto wayaka,+Ndipo udzayaka mpaka kukafika ku Manda,* malo a pansi penipeni.+Udzanyeketsa dziko lapansi ndi zipatso zake,+Ndi kuyatsa maziko a mapiri.+
16 Kenako, ndinamva mawu ofuula+ ochokera m’malo opatulika akuuza angelo 7 aja kuti: “Pitani, kathireni mbale 7 za mkwiyo+ wa Mulunguzo kudziko lapansi.”