Chivumbulutso 16:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mngelo wachinayi+ anathira mbale yake padzuwa. Ndipo dzuwa linaloledwa kutentha+ anthu ndi moto.