Deuteronomo 4:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ndipo Yehova adzakubalalitsani pakati pa anthu a mitundu ina,+ ndipo mudzatsala ochepa+ m’mayiko a mitundu imene Yehova adzakuingitsiraniko. Deuteronomo 28:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Udzatumikira adani ako+ amene Yehova adzawatuma kuti akuukire. Udzawatumikira uli ndi njala,+ ludzu, usiwa ndiponso ukusowa china chilichonse. Adzakuveka goli lachitsulo m’khosi lako kufikira atakufafaniza.+ Yeremiya 42:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Amuna onse amene atsimikiza mtima kukakhala ku Iguputo monga alendo ndiwo adzafa ndi lupanga, njala yaikulu ndi mliri.+ Pakati pawo sipadzapezeka wopulumuka kapena wothawa chifukwa ndidzawagwetsera tsoka.”’+
27 Ndipo Yehova adzakubalalitsani pakati pa anthu a mitundu ina,+ ndipo mudzatsala ochepa+ m’mayiko a mitundu imene Yehova adzakuingitsiraniko.
48 Udzatumikira adani ako+ amene Yehova adzawatuma kuti akuukire. Udzawatumikira uli ndi njala,+ ludzu, usiwa ndiponso ukusowa china chilichonse. Adzakuveka goli lachitsulo m’khosi lako kufikira atakufafaniza.+
17 Amuna onse amene atsimikiza mtima kukakhala ku Iguputo monga alendo ndiwo adzafa ndi lupanga, njala yaikulu ndi mliri.+ Pakati pawo sipadzapezeka wopulumuka kapena wothawa chifukwa ndidzawagwetsera tsoka.”’+