Deuteronomo 28:64 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 64 “Yehova adzakumwazani mwa anthu a mitundu yonse kuchokera kumalekezero ena a dziko mpaka kumalekezero enanso a dziko.+ Kumeneko mukatumikira milungu ina imene inuyo kapena makolo anu simunaidziwe, milungu yamtengo ndi milungu yamwala.+ Nehemiya 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Chonde, kumbukirani+ mawu amene munauza mtumiki wanu Mose kuti, ‘Mukadzachita zinthu mosakhulupirika, ndidzakumwazani pakati pa anthu a mitundu ina.+ Ezekieli 12:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndikadzawabalalitsira ku mitundu ina ya anthu ndi kumayiko ena, iwo adzadziwa kuti ine ndine Yehova.+
64 “Yehova adzakumwazani mwa anthu a mitundu yonse kuchokera kumalekezero ena a dziko mpaka kumalekezero enanso a dziko.+ Kumeneko mukatumikira milungu ina imene inuyo kapena makolo anu simunaidziwe, milungu yamtengo ndi milungu yamwala.+
8 “Chonde, kumbukirani+ mawu amene munauza mtumiki wanu Mose kuti, ‘Mukadzachita zinthu mosakhulupirika, ndidzakumwazani pakati pa anthu a mitundu ina.+
15 Ndikadzawabalalitsira ku mitundu ina ya anthu ndi kumayiko ena, iwo adzadziwa kuti ine ndine Yehova.+