Deuteronomo 28:64 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 64 Yehova adzakubalalitsirani pakati pa mitundu yonse, kuchokera kumalekezero a dziko mpaka kumalekezero ena a dziko.+ Kumeneko mudzatumikira milungu yamtengo komanso milungu yamwala, imene inuyo kapena makolo anu sanaidziwe.+
64 Yehova adzakubalalitsirani pakati pa mitundu yonse, kuchokera kumalekezero a dziko mpaka kumalekezero ena a dziko.+ Kumeneko mudzatumikira milungu yamtengo komanso milungu yamwala, imene inuyo kapena makolo anu sanaidziwe.+