Salimo 9:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Yehova amadziwika ndi ziweruzo zimene amapereka.+Woipa wakodwa mumsampha wa ntchito ya manja ake.+Higayoni.* [Seʹlah.] Ezekieli 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndidzawatambasulira dzanja langa powalanga+ ndipo dziko lawo ndidzalisandutsa bwinja. Malo awo onse okhala adzakhala bwinja loipa kuposa chipululu cha Dibula, ndipo iwo adzadziwa kuti ine ndine Yehova.’”
16 Yehova amadziwika ndi ziweruzo zimene amapereka.+Woipa wakodwa mumsampha wa ntchito ya manja ake.+Higayoni.* [Seʹlah.]
14 Ndidzawatambasulira dzanja langa powalanga+ ndipo dziko lawo ndidzalisandutsa bwinja. Malo awo onse okhala adzakhala bwinja loipa kuposa chipululu cha Dibula, ndipo iwo adzadziwa kuti ine ndine Yehova.’”