Deuteronomo 4:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Kumeneko mudzatumikira milungu+ yopangidwa ndi manja a anthu, milungu ya mtengo ndi mwala,+ imene siingaone, kumva, kudya kapena kununkhiza.+ Deuteronomo 28:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Yehova adzakuyendetsa+ pamodzi ndi mfumu+ yako imene udzadziikira, kukupititsa ku mtundu umene iweyo kapena makolo ako simunaudziwe. Kumeneko udzatumikira milungu ina, yamtengo kapena yamwala.+ Yeremiya 16:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho ndidzakutayani kunja kukuchotsani m’dziko lino+ ndi kukupititsani kudziko limene inu ngakhalenso makolo anu sanalidziwe.+ Kumeneko mukatumikira milungu ina+ usana ndi usiku chifukwa sindidzakumverani chifundo.”’
28 Kumeneko mudzatumikira milungu+ yopangidwa ndi manja a anthu, milungu ya mtengo ndi mwala,+ imene siingaone, kumva, kudya kapena kununkhiza.+
36 Yehova adzakuyendetsa+ pamodzi ndi mfumu+ yako imene udzadziikira, kukupititsa ku mtundu umene iweyo kapena makolo ako simunaudziwe. Kumeneko udzatumikira milungu ina, yamtengo kapena yamwala.+
13 Choncho ndidzakutayani kunja kukuchotsani m’dziko lino+ ndi kukupititsani kudziko limene inu ngakhalenso makolo anu sanalidziwe.+ Kumeneko mukatumikira milungu ina+ usana ndi usiku chifukwa sindidzakumverani chifundo.”’