Salimo 119:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Kumbukirani mawu amene munandiuza ine mtumiki wanu,+Mawu amene ndikuwayembekezera malinga ndi lonjezo lanu.+ Luka 1:72 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 72 Kuchitira chifundo makolo athu akale ndi kukumbukira pangano lake loyera,+
49 Kumbukirani mawu amene munandiuza ine mtumiki wanu,+Mawu amene ndikuwayembekezera malinga ndi lonjezo lanu.+