Deuteronomo 32:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pakuti pa kukwiya kwanga moto wayaka,+Ndipo udzayaka mpaka kukafika ku Manda,* malo a pansi penipeni.+Udzanyeketsa dziko lapansi ndi zipatso zake,+Ndi kuyatsa maziko a mapiri.+ Salimo 110:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yehova amene ali kudzanja lako lamanja+Adzaphwanyaphwanya mafumu pa tsiku la mkwiyo wake.+
22 Pakuti pa kukwiya kwanga moto wayaka,+Ndipo udzayaka mpaka kukafika ku Manda,* malo a pansi penipeni.+Udzanyeketsa dziko lapansi ndi zipatso zake,+Ndi kuyatsa maziko a mapiri.+