Salimo 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kodi ndidzalimbana ndi masautso anga kufikira liti?Kodi masiku a moyo wanga adzakhala odzaza ndi chisoni kufikira liti?Kodi mdani wanga adzadzikweza pamaso panga kufikira liti?+ Salimo 79:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Anthu oyandikana nafe akutitonza,+Anthu otizungulira akutinyoza ndi kutiseka.+
2 Kodi ndidzalimbana ndi masautso anga kufikira liti?Kodi masiku a moyo wanga adzakhala odzaza ndi chisoni kufikira liti?Kodi mdani wanga adzadzikweza pamaso panga kufikira liti?+