2 Mafumu 19:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Tcherani khutu lanu, inu Yehova, mumve.+ Tsegulani maso anu,+ inu Yehova, muone, ndipo imvani mawu a Senakeribu amene watumiza kudzatonza nawo+ Mulungu wamoyo.
16 Tcherani khutu lanu, inu Yehova, mumve.+ Tsegulani maso anu,+ inu Yehova, muone, ndipo imvani mawu a Senakeribu amene watumiza kudzatonza nawo+ Mulungu wamoyo.