2 Mbiri 29:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pakuti makolo athu achita zosakhulupirika+ ndipo achita zoipa pamaso pa Yehova Mulungu wathu.+ Iwo anamusiya+ n’kufulatira chihema chopatulika cha Yehova+ n’kulozetsako nkhongo. Aefeso 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Inde, tonsefe pa nthawi inayake pamene tinali pakati pawo, tinali kukhala motsatira zilakolako za thupi lathu.+ Tinali kuchita zofuna za thupi+ ndi maganizo, ndipo mwachibadwa tinali ana oyenera kulandira mkwiyo wa Mulungu,+ mofanana ndi ena onse.
6 Pakuti makolo athu achita zosakhulupirika+ ndipo achita zoipa pamaso pa Yehova Mulungu wathu.+ Iwo anamusiya+ n’kufulatira chihema chopatulika cha Yehova+ n’kulozetsako nkhongo.
3 Inde, tonsefe pa nthawi inayake pamene tinali pakati pawo, tinali kukhala motsatira zilakolako za thupi lathu.+ Tinali kuchita zofuna za thupi+ ndi maganizo, ndipo mwachibadwa tinali ana oyenera kulandira mkwiyo wa Mulungu,+ mofanana ndi ena onse.