Salimo 86:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Inu Yehova, tcherani khutu ku pemphero langa.+Ndipo mvetserani mawu a kuchonderera kwanga.+ Salimo 130:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Imvani mawu anga Yehova.+Makutu anu amve mawu anga ochonderera.+