1 Mafumu 8:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 “Anthu anu Aisiraeli akagonja kwa adani+ awo chifukwa choti anali kukuchimwirani,+ ndiyeno akabwerera kwa inu+ n’kutamanda dzina lanu+ ndi kupemphera+ ndiponso kupempha kwa inu kuti muwachitire chifundo m’nyumba ino,+
33 “Anthu anu Aisiraeli akagonja kwa adani+ awo chifukwa choti anali kukuchimwirani,+ ndiyeno akabwerera kwa inu+ n’kutamanda dzina lanu+ ndi kupemphera+ ndiponso kupempha kwa inu kuti muwachitire chifundo m’nyumba ino,+