2 Mbiri 6:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Maso anu akhale akuyang’ana+ nyumba ino usana ndi usiku. Akhale akuyang’ana malo amene munanena kuti mudzaikako dzina lanu,+ mwa kumvetsera pemphero limene mtumiki wanu akupemphera atayang’ana malo ano.+
20 Maso anu akhale akuyang’ana+ nyumba ino usana ndi usiku. Akhale akuyang’ana malo amene munanena kuti mudzaikako dzina lanu,+ mwa kumvetsera pemphero limene mtumiki wanu akupemphera atayang’ana malo ano.+